Mateyu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.+ Luka 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atamwaza maso uku ndi uku kuwayang’ana onsewo, anauza munthu uja kuti: “Tambasula dzanja lako.” Munthuyo anachitadi zimenezo, ndipo dzanja lakelo linakhalanso labwinobwino.+
13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.+
10 Atamwaza maso uku ndi uku kuwayang’ana onsewo, anauza munthu uja kuti: “Tambasula dzanja lako.” Munthuyo anachitadi zimenezo, ndipo dzanja lakelo linakhalanso labwinobwino.+