Mateyu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.+ Maliko 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yesu anawayang’ana mokwiya ndi kumva chisoni kwambiri chifukwa cha kuuma mtima kwawo.+ Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhala labwinobwino.+
13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.+
5 Pamenepo Yesu anawayang’ana mokwiya ndi kumva chisoni kwambiri chifukwa cha kuuma mtima kwawo.+ Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi, ndipo linakhala labwinobwino.+