Mateyu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Yesu anayamba ulendo kuchoka kukachisiko. Kenako ophunzira ake anabwera pafupi naye kuti amuonetse nyumba za pakachisipo.+ Luka 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nthawi ina, anthu ena anali kulankhula za kachisi, mmene anam’kongoletsera ndi miyala yochititsa kaso komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu.+
24 Tsopano Yesu anayamba ulendo kuchoka kukachisiko. Kenako ophunzira ake anabwera pafupi naye kuti amuonetse nyumba za pakachisipo.+
5 Nthawi ina, anthu ena anali kulankhula za kachisi, mmene anam’kongoletsera ndi miyala yochititsa kaso komanso mphatso zoperekedwa kwa Mulungu.+