Mateyu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Yesu anayamba ulendo kuchoka kukachisiko. Kenako ophunzira ake anabwera pafupi naye kuti amuonetse nyumba za pakachisipo.+ Maliko 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Yesu anali kutuluka m’kachisi, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Mphunzitsi, taonani mmene miyala ndi nyumbazi zikuonekera!”+
24 Tsopano Yesu anayamba ulendo kuchoka kukachisiko. Kenako ophunzira ake anabwera pafupi naye kuti amuonetse nyumba za pakachisipo.+
13 Pamene Yesu anali kutuluka m’kachisi, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Mphunzitsi, taonani mmene miyala ndi nyumbazi zikuonekera!”+