Yesaya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+ Zekariya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndiyeno magawo awiri mwa magawo atatu a anthu a m’dziko lonseli adzaphedwa.+ Koma gawo lachitatu la anthuwo lidzatsalamo,”+ watero Yehova.
9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
8 “Ndiyeno magawo awiri mwa magawo atatu a anthu a m’dziko lonseli adzaphedwa.+ Koma gawo lachitatu la anthuwo lidzatsalamo,”+ watero Yehova.