Mateyu 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha. Luka 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+
2 Komanso ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yabwino yophera Yesu,+ pakuti anali kuopa anthu.+