Yona 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona,+ moti Yona anakhala m’mimba mwa nsomba masiku atatu, usana ndi usiku.+ Mateyu 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Maliko 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwo akam’chitira chipongwe, kum’lavulira, kum’kwapula ndi kumupha, koma patapita masiku atatu, adzauka.”+ Luka 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anati: “Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri. Iye adzakanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno adzaphedwa,+ koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+
17 Tsopano Yehova anatumiza chinsomba chachikulu kuti chikameze Yona,+ moti Yona anakhala m’mimba mwa nsomba masiku atatu, usana ndi usiku.+
19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+
34 Iwo akam’chitira chipongwe, kum’lavulira, kum’kwapula ndi kumupha, koma patapita masiku atatu, adzauka.”+
22 Kenako anati: “Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri. Iye adzakanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno adzaphedwa,+ koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+