Salimo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+ Yesaya 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+ Yesaya 53:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.+ Ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mibadwo ya makolo ake?+ Pakuti iye anadulidwa+ m’dziko la amoyo.+ Chifukwa cha zolakwa+ za anthu anga, iye anakwapulidwa.+ Danieli 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye adzagonjetsa magulu ankhondo+ okhala ngati madzi osefukira, ndipo magulu ankhondowo adzawonongedwa.+ Mtsogoleri+ wa pangano+ nayenso+ adzawonongedwa.
15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+
5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+
8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.+ Ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mibadwo ya makolo ake?+ Pakuti iye anadulidwa+ m’dziko la amoyo.+ Chifukwa cha zolakwa+ za anthu anga, iye anakwapulidwa.+
22 Iye adzagonjetsa magulu ankhondo+ okhala ngati madzi osefukira, ndipo magulu ankhondowo adzawonongedwa.+ Mtsogoleri+ wa pangano+ nayenso+ adzawonongedwa.