Ekisodo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ukapeza ng’ombe kapena bulu wa mdani wako atasochera, um’bweze ndithu kwa mwiniwake.+ Miyambo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ngati munthu wodana nawe ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse madzi akumwa,+ Aroma 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse chakumwa.+ Pakuti mwa kutero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”+
21 Ngati munthu wodana nawe ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse madzi akumwa,+
20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse chakumwa.+ Pakuti mwa kutero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”+