Mlaliki 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Mulungu woona adzaweruza ntchito iliyonse ndiponso chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati zili zabwino kapena zoipa.+ Mateyu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho musawaope, pakuti palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+ Maliko 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti chilichonse chobisidwa chidzaululika. Chilichonse chimene chimasungidwa mwachinsinsi kwambiri chidzadziwika.+ Luka 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chilichonse chobisidwa+ chidzaonekera poyera. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika ndi kuululika.+ 1 Akorinto 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+
14 Pakuti Mulungu woona adzaweruza ntchito iliyonse ndiponso chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati zili zabwino kapena zoipa.+
26 Choncho musawaope, pakuti palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+
22 Pakuti chilichonse chobisidwa chidzaululika. Chilichonse chimene chimasungidwa mwachinsinsi kwambiri chidzadziwika.+
17 Chilichonse chobisidwa+ chidzaonekera poyera. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika ndi kuululika.+
5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+