Yohane 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mungakhulupirire bwanji, pamene mumalandira ulemerero+ kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kupeza ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+ Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+ 2 Akorinto 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti wodzikweza yekha si amene amavomerezedwa,+ koma amene Yehova+ wamuvomereza.+
44 Mungakhulupirire bwanji, pamene mumalandira ulemerero+ kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kupeza ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+
29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+