Genesis 41:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Tsopano mufunefune munthu wozindikira ndi wanzeru, ndipo mumuike kukhala woyang’anira dziko la Iguputo.+ Deuteronomo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+
33 “Tsopano mufunefune munthu wozindikira ndi wanzeru, ndipo mumuike kukhala woyang’anira dziko la Iguputo.+
13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+