Mateyu 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kuyambira pamenepo, Yesu Khristu anayamba kuuza ophunzira ake kuti n’koyenera kuti iye apite ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+ Aroma 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye chifukwa chake Khristu anafa n’kukhalanso ndi moyo,+ kuti akhale Ambuye wa akufa+ ndiponso wa amoyo.+ 1 Akorinto 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Wopusa iwe! Chimene wabzala sichikhala ndi moyo pokhapokha chitafa kaye.+
21 Kuyambira pamenepo, Yesu Khristu anayamba kuuza ophunzira ake kuti n’koyenera kuti iye apite ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+
9 Ndiye chifukwa chake Khristu anafa n’kukhalanso ndi moyo,+ kuti akhale Ambuye wa akufa+ ndiponso wa amoyo.+