2 Akorinto 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mtima wanga sunakhazikike chifukwa Tito+ m’bale wanga sindinamupeze. Ndiye ndinatsanzikana ndi abale kumeneko, n’kupita ku Makedoniya.+
13 mtima wanga sunakhazikike chifukwa Tito+ m’bale wanga sindinamupeze. Ndiye ndinatsanzikana ndi abale kumeneko, n’kupita ku Makedoniya.+