Genesis 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Yehova anakhalabe ndi Yosefe, ndipo iye anakhala wopambana m’zochita zake zonse.+ Anakhalanso munthu waudindo m’nyumba ya mbuye wake, Mwiguputoyo.
2 Koma Yehova anakhalabe ndi Yosefe, ndipo iye anakhala wopambana m’zochita zake zonse.+ Anakhalanso munthu waudindo m’nyumba ya mbuye wake, Mwiguputoyo.