-
2 Petulo 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 ndipo akudzilakwira okha+ monga mphoto yawo ya kuchita zoipa.+
Iwo amaona kuti kuchita masana zinthu zokhutiritsa chilakolako cha thupi lawo n’kosangalatsa.+ Anthu amenewa ali ngati mawanga ndi zilema pakati panu, ndipo amakondwera kwadzaoneni akamakuphunzitsani zinthu zonyenga pamene akudya nanu limodzi.+
-