1 Akorinto 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukupulumutsidwa+ ndi uthenga wabwino umenewo ngati mwaugwiritsitsa. Popanda kutero, ndiye kuti munakhala okhulupirira pachabe,+ malinga ndi mawu amene ndinakuuzani polengeza uthengawo kwa inu.
2 Mukupulumutsidwa+ ndi uthenga wabwino umenewo ngati mwaugwiritsitsa. Popanda kutero, ndiye kuti munakhala okhulupirira pachabe,+ malinga ndi mawu amene ndinakuuzani polengeza uthengawo kwa inu.