-
1 Samueli 30:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zimenezi zinam’vutitsa maganizo kwambiri Davide+ chifukwanso anthu anali kukambirana zom’ponya miyala.+ Anthuwo anali kukambirana zimenezi chifukwa aliyense wa iwo anali wokwiya kwambiri+ poona zimene zachitikira ana awo aamuna ndi ana awo aakazi. Choncho, Davide anadzilimbitsa mwa Yehova Mulungu wake.+
-