Agalatiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaleke kunyamulirana zolemetsa.+ Mukatero mudzakhala mukukwaniritsa chilamulo cha Khristu.+ Aheberi 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumbukirani amene ali m’ndende+ ngati kuti mwamangidwa nawo limodzi.+ Kumbukiraninso amene akuzunzidwa,+ popeza inunso mudakali m’thupi lanyama. 1 Petulo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma inu khalani olimba+ m’chikhulupiriro ndipo mulimbane naye, podziwa kuti anzanunso m’gulu lonse la abale anu m’dzikoli akukumana ndi masautso ngati omwewo.+
3 Kumbukirani amene ali m’ndende+ ngati kuti mwamangidwa nawo limodzi.+ Kumbukiraninso amene akuzunzidwa,+ popeza inunso mudakali m’thupi lanyama.
9 Koma inu khalani olimba+ m’chikhulupiriro ndipo mulimbane naye, podziwa kuti anzanunso m’gulu lonse la abale anu m’dzikoli akukumana ndi masautso ngati omwewo.+