Mateyu 25:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndinali wamaliseche+ koma inu munandiveka. Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali m’ndende+ koma inu munabwera kudzandiona.’ Akolose 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo+ amene andimanga nawo kundende kuno. Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.
36 Ndinali wamaliseche+ koma inu munandiveka. Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali m’ndende+ koma inu munabwera kudzandiona.’
18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo+ amene andimanga nawo kundende kuno. Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.