Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+ Afilipi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+
5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+