Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+ Miyambo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+
14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+