1 Akorinto 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamanane,+ kupatulapo ngati mwagwirizana kuimitsa kaye mangawawo kwa nthawi yodziwika,+ kuti muthere nthawi pa kupemphera, kenako mukhalenso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kumakuyesani+ mukalephera kudzigwira.+ Yakobo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.
5 Musamanane,+ kupatulapo ngati mwagwirizana kuimitsa kaye mangawawo kwa nthawi yodziwika,+ kuti muthere nthawi pa kupemphera, kenako mukhalenso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kumakuyesani+ mukalephera kudzigwira.+
2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.