-
Yuda 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndatero chifukwa chakuti anthu ena alowa mozemba pakati pathu.+ Anthu amenewa Malemba anawasonyezeratu kalekale+ kuti adzaweruzidwa.+ Iwo ndiwo anthu osaopa Mulungu+ amene atenga kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu kukhala chifukwa chochitira khalidwe lotayirira,+ ndipo akhala osakhulupirika+ kwa Ambuye wathu mmodzi yekha+ amene anatigula,+ Yesu Khristu.
-