Aefeso 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino. Aheberi 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo,+ mpingo wa iwo amene analembedwa+ kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse,+ ndiponso kuli moyo wauzimu wa olungama+ amene akhala angwiro.+
6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino.
23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo,+ mpingo wa iwo amene analembedwa+ kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse,+ ndiponso kuli moyo wauzimu wa olungama+ amene akhala angwiro.+