Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+ Salimo 94:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyamukani inu Woweruza dziko lapansi.+Perekani chilango kwa anthu odzikweza.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+
25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+
22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+