Machitidwe 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘“Ndipo m’masiku otsiriza,” akutero Mulungu, “ndidzatsanulira mbali ya mzimu wanga+ pa anthu osiyanasiyana, ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera. Anyamata anu adzaona masomphenya, ndipo amuna achikulire adzalota maloto.+ Aroma 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu+ umatithandiza pa zofooka zathu.+ Pakuti chimene tiyenera kupempherera monga mmene tiyenera kupemphera sitikuchidziwa,+ koma mzimu+ umachonderera m’malo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.
17 ‘“Ndipo m’masiku otsiriza,” akutero Mulungu, “ndidzatsanulira mbali ya mzimu wanga+ pa anthu osiyanasiyana, ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera. Anyamata anu adzaona masomphenya, ndipo amuna achikulire adzalota maloto.+
26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu+ umatithandiza pa zofooka zathu.+ Pakuti chimene tiyenera kupempherera monga mmene tiyenera kupemphera sitikuchidziwa,+ koma mzimu+ umachonderera m’malo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.