Aroma 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+ 1 Akorinto 15:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo.
29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba+ anawasankhiratu+ kuti adzakhale ofanana+ ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+
49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo.