7 N’zoyenera kwa ineyo kuganizira nonsenu mwa njira imeneyi, pakuti inu ndinu apamtima panga,+ ndiponso nonsenu ndinu ogawana+ nane m’kukoma mtima kwakukulu, m’maunyolo anga m’ndende,+ ndi pa kuteteza+ uthenga wabwino ndi kukhazikitsa mwalamulo ntchito ya uthenga wabwino.+