Miyambo 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndinadutsa pamunda pa munthu waulesi+ ndiponso pamunda wa mpesa wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+ 1 Atesalonika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.
30 Ndinadutsa pamunda pa munthu waulesi+ ndiponso pamunda wa mpesa wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+
14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.