Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+ Aefeso 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza+ moona mtima, monga mmene mumachitira ndi Khristu. Akolose 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu akapolo, muzimvera ambuye anu a padziko lapansi+ pa zinthu zonse, osati mwachiphamaso ngati ofuna kukondweretsa+ anthu, koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.+
7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+
5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza+ moona mtima, monga mmene mumachitira ndi Khristu.
22 Inu akapolo, muzimvera ambuye anu a padziko lapansi+ pa zinthu zonse, osati mwachiphamaso ngati ofuna kukondweretsa+ anthu, koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.+