Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+
16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+