Mateyu 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mudzawazindikira ndi zipatso zawo.+ Anthu sathyola mphesa paminga kapena nkhuyu pamitula, amatero kodi?+ 2 Timoteyo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+
16 Mudzawazindikira ndi zipatso zawo.+ Anthu sathyola mphesa paminga kapena nkhuyu pamitula, amatero kodi?+
2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzimva, odzikweza, onyoza, osamvera makolo,+ osayamika, osakhulupirika,+