1 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipotu, si kuti mawu a Yehova+ ochokera kwa inu amveka ku Makedoniya ndi ku Akaya kokha ayi, koma kwina kulikonse chikhulupiriro+ chanu mwa Mulungu chafalikira,+ moti ife sitikufunika kunenapo kanthu.
8 Ndipotu, si kuti mawu a Yehova+ ochokera kwa inu amveka ku Makedoniya ndi ku Akaya kokha ayi, koma kwina kulikonse chikhulupiriro+ chanu mwa Mulungu chafalikira,+ moti ife sitikufunika kunenapo kanthu.