Aheberi 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mwa chikhulupiriro, pamene Abulahamu anayesedwa,+ zinali ngati wapereka kale Isaki nsembe. Choncho munthu ameneyu, amene analandira malonjezo mokondwera, anali wokonzeka kupereka nsembe mwana wake wobadwa yekha.+
17 Mwa chikhulupiriro, pamene Abulahamu anayesedwa,+ zinali ngati wapereka kale Isaki nsembe. Choncho munthu ameneyu, amene analandira malonjezo mokondwera, anali wokonzeka kupereka nsembe mwana wake wobadwa yekha.+