Aroma 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tikudziwa kuti pamene tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa,+ sadzafanso.+ Imfa sikuchitanso ufumu pa iye. 1 Timoteyo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye yekha ndiye amene ali ndi moyo wosakhoza kufa,+ amene amakhala m’kuwala kosafikirika.+ Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu+ ndipo mphamvu zake zikhalebe kosatha. Ame. Chivumbulutso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+
9 Tikudziwa kuti pamene tsopano Khristu waukitsidwa kwa akufa,+ sadzafanso.+ Imfa sikuchitanso ufumu pa iye.
16 Iye yekha ndiye amene ali ndi moyo wosakhoza kufa,+ amene amakhala m’kuwala kosafikirika.+ Palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene anamuonapo kapena amene angamuone.+ Iye apatsidwe ulemu+ ndipo mphamvu zake zikhalebe kosatha. Ame.
18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo kwamuyaya,+ ndipo ndili ndi makiyi a imfa+ ndi a Manda.*+