Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+ Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ngati kuti ndaziphimba ndi mtambo,+ ndi machimo ako ngati kuti ndawaphimba ndi mitambo yambiri. Bwerera kwa ine,+ ndipo ine ndikuwombola.+