1 Akorinto 15:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa. 2 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+ 1 Petulo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo m’busa wamkulu+ akadzaonekera, mudzalandira mphoto* yosafwifwa,+ yaulemerero.+
53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa.
10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+