Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo. Chivumbulutso 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzamupatsanso nthanda.*+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+
17 Ndidzamuona,+ koma si nthawi ino;Ndidzam’penya, koma si panopo.Ndithu nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu idzatulukadi mu Isiraeli.+Ndipo iye adzaphwanya chipumi cha Mowabu+Ndi chigaza cha ana onse ankhondo.
16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+