Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 317-318 Nsanja ya Olonda,4/1/2000, tsa. 148/15/1994, tsa. 31
16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+