Tito 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amanena poyera kuti amadziwa Mulungu,+ koma amamukana ndi zochita zawo+ chifukwa ndi onyansa ndi osamvera, ndipo ndi osayenerera+ ntchito iliyonse yabwino. 1 Yohane 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amene amanena kuti: “Ine ndikumudziwa,”+ koma sasunga malamulo ake,+ ameneyo ndi wabodza, ndipo mwa munthu ameneyo mulibe choonadi.+
16 Amanena poyera kuti amadziwa Mulungu,+ koma amamukana ndi zochita zawo+ chifukwa ndi onyansa ndi osamvera, ndipo ndi osayenerera+ ntchito iliyonse yabwino.
4 Munthu amene amanena kuti: “Ine ndikumudziwa,”+ koma sasunga malamulo ake,+ ameneyo ndi wabodza, ndipo mwa munthu ameneyo mulibe choonadi.+