Chivumbulutso 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mkaziyo anabereka mwana wamwamuna,+ mnyamata amene adzakusa mitundu yonse ndi ndodo yachitsulo.+ Ndipo mwana wakeyo anatengedwa msangamsanga n’kupititsidwa kwa Mulungu ndi kumpando wake wachifumu.+ Chivumbulutso 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga+ lalitali lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu, ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Iye anali kupondapondanso m’chopondera mphesa+ cha mkwiyo waukulu wa Mulungu+ Wamphamvuyonse.
5 Mkaziyo anabereka mwana wamwamuna,+ mnyamata amene adzakusa mitundu yonse ndi ndodo yachitsulo.+ Ndipo mwana wakeyo anatengedwa msangamsanga n’kupititsidwa kwa Mulungu ndi kumpando wake wachifumu.+
15 M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga+ lalitali lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu, ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Iye anali kupondapondanso m’chopondera mphesa+ cha mkwiyo waukulu wa Mulungu+ Wamphamvuyonse.