Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo adzanena kuti: “Inetu ndakhazika mfumu yanga+Pa Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”+ Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+