Salimo 89:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Inenso ndidzamuika kukhala mwana woyamba kubadwa,+Ndiponso mfumu yaikulu pa mafumu onse a padziko lapansi.+ 1 Timoteyo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Wachimwemwe ndi Wamphamvu yekhayo,+ iye amene ali Mfumu+ ya olamulira monga mafumu ndi Mbuye+ wa olamulira monga ambuye, adzaonekera pa nthawi zake zoikidwiratu.+ Chivumbulutso 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamalaya ake akunja, ngakhale pantchafu yake, anali ndi dzina lolembedwa lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+
27 Inenso ndidzamuika kukhala mwana woyamba kubadwa,+Ndiponso mfumu yaikulu pa mafumu onse a padziko lapansi.+
15 Wachimwemwe ndi Wamphamvu yekhayo,+ iye amene ali Mfumu+ ya olamulira monga mafumu ndi Mbuye+ wa olamulira monga ambuye, adzaonekera pa nthawi zake zoikidwiratu.+
16 Pamalaya ake akunja, ngakhale pantchafu yake, anali ndi dzina lolembedwa lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+