Genesis 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+ Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo.
17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+
3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo.