Mateyu 22:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 ‘Yehova wauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja kufikira nditaika adani ako kunsi kwa mapazi ako”’?+ Machitidwe 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”’+ 1 Akorinto 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti ayenera kulamulira monga mfumu kufikira Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi+ ake. Aheberi 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma kodi ndi mngelo uti amene anamuuzapo kuti: “Khala kudzanja langa lamanja, kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako”?+ Aheberi 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuyambira pamenepo, akuyembekezera kufikira pamene adani ake adzaikidwe monga chopondapo mapazi ake.+
44 ‘Yehova wauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja kufikira nditaika adani ako kunsi kwa mapazi ako”’?+
13 Koma kodi ndi mngelo uti amene anamuuzapo kuti: “Khala kudzanja langa lamanja, kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako”?+
13 Kuyambira pamenepo, akuyembekezera kufikira pamene adani ake adzaikidwe monga chopondapo mapazi ake.+