Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani? Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pamenepa? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+ Aheberi 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+
27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani?
10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’
6 Tikhale olimba mtima ndithu ndipo tinene kuti: “Yehova* ndi amene amandithandiza. Sindidzaopa. Munthu angandichite chiyani?”+