Yobu 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi, Mulungu sachita zoipa,+Ndipo Wamphamvuyonse sakhotetsa chilungamo.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+
22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+