Levitiko 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ Yakobo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu Wopereka Malamulo komanso Woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani kuti uziweruza mnzako?+
12 Komatu Wopereka Malamulo komanso Woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani kuti uziweruza mnzako?+