Genesis 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulamu anayankha kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo Eliezere wa ku Damasiko ndi amene adzatenge katundu wanga yense monga cholowa chake.”+ Genesis 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yehova anamuyankha kuti: “Munthu ameneyu sadzatenga katundu wako monga cholowa chake, koma mwana wako ndi amene adzatenge kuti chikhale cholowa chake.”+ Agalatiya 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi amene ndi mfulu.”+
2 Abulamu anayankha kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo Eliezere wa ku Damasiko ndi amene adzatenge katundu wanga yense monga cholowa chake.”+
4 Koma Yehova anamuyankha kuti: “Munthu ameneyu sadzatenga katundu wako monga cholowa chake, koma mwana wako ndi amene adzatenge kuti chikhale cholowa chake.”+
30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi amene ndi mfulu.”+